كتاب أسئلة الطفل الإيمانية باللغة السواحلية

 

كتاب أسئلة الطفل الإيمانية:

نماذج عملية للإجابة عن أسئلة الأطفال المتعلقة بأركان الإيمان

 

 

MAFUNSO A ANA pA CHIKHULUPILIRO

 

Bukuli lagawidwa m’magawo awiri : gawo loyamba (zokhudza maphunziro

a chikhulupiliro ), m’menemo muli maziko ambiri omwe angathandize

makolo kuphunzitsa ana awo – mu chifuniro cha Allah -,

pomwe gawo la chiwiri likuzungulira pa (zitsanzo zochitika pakayankhidwe

ka mafunso a ana okhudza chikhululupiliro) m’menemo tiyankhamo

mafunso amene ali otchuka kwambiri pakati pa ana amisinkhu yosiyana

siyana, makamaka omwe akukhudzana ndi msichi zachikhulupiliro

zisanu ndi imodzi (6) ndipo tafotokozamo momveka bwino m’mene tingayankhire

mafunso ngati amenewa